Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Yehova anapitiriza kuuza Mose kuti: “Ulembe mawuwa+ chifukwa ine ndikuchita pangano ndi iwe komanso Isiraeli mogwirizana ndi mawu amenewa.”+

  • Deuteronomo 31:24-26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mose atangomaliza kulemba mawu onse a Chilamulo ichi mʼbuku,+ 25 Mose analamula Alevi amene amanyamula likasa la pangano la Yehova kuti: 26 “Tengani buku ili la Chilamulo+ ndipo muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, ndipo lidzakhala mboni ya Mulungu yokutsutsani.

  • Aheberi 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho malamulo oyambawo akuchotsedwa chifukwa ndi operewera komanso osathandiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena