Aroma 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo lamulo limene linkafunika kunditsogolera kuti ndipeze moyo,+ linanditsogolera ku imfa. Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+
10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+