4 Choncho ine, amene ndili mʼndende+ chifukwa cha Ambuye, ndikukuchondererani kuti muzichita zinthu mogwirizana+ ndi kuitana kumene anakuitanani. 2 Nthawi zonse muzichita zinthu modzichepetsa,+ mofatsa, moleza mtima+ ndiponso muzilolerana chifukwa cha chikondi.+