Aroma 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuchokera kumwamba, Mulungu akusonyeza mkwiyo wake+ kwa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zoipa amene akuchititsa kuti choonadi chisadziwike.+
18 Kuchokera kumwamba, Mulungu akusonyeza mkwiyo wake+ kwa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zoipa amene akuchititsa kuti choonadi chisadziwike.+