Yohane 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala. Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha ndipo masana ayandikira. Choncho tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+ Aefeso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala.
36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani kuti mukukhulupirira kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka nʼkukabisala.
12 Usiku uli pafupi kutha ndipo masana ayandikira. Choncho tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+
8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala.