Aroma 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tiyeni tikhale ndi khalidwe loyenera+ ngati anthu amene akuchita zinthu masana. Tizipewa maphwando oipa,* kumwa mwauchidakwa,* chiwerewere, khalidwe lopanda manyazi,*+ mikangano ndiponso nsanje.+
13 Tiyeni tikhale ndi khalidwe loyenera+ ngati anthu amene akuchita zinthu masana. Tizipewa maphwando oipa,* kumwa mwauchidakwa,* chiwerewere, khalidwe lopanda manyazi,*+ mikangano ndiponso nsanje.+