Yohane 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Zimene Atate wanga akufuna ndi zoti aliyense wovomereza Mwana komanso kumukhulupirira akhale ndi moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa+ pa tsiku lomaliza.” Yohane 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, komanso chifukwa choti mwakhulupirira, mukhale ndi moyo mʼdzina lake.+
40 Zimene Atate wanga akufuna ndi zoti aliyense wovomereza Mwana komanso kumukhulupirira akhale ndi moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa+ pa tsiku lomaliza.”
31 Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, komanso chifukwa choti mwakhulupirira, mukhale ndi moyo mʼdzina lake.+