Aroma 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mʼmalo molemekeza Mulungu yemwe sangafe, iwo amalemekeza zifaniziro za anthu omwe amafa komanso zifaniziro za mbalame, nyama za miyendo 4 ndiponso nyama zokwawa.+
23 Mʼmalo molemekeza Mulungu yemwe sangafe, iwo amalemekeza zifaniziro za anthu omwe amafa komanso zifaniziro za mbalame, nyama za miyendo 4 ndiponso nyama zokwawa.+