Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Timoteyo 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma uzipewa nkhani zonama zosalemekeza Mulungu+ ngati zimene amayi ena okalamba amakamba. Mʼmalomwake, uzidziphunzitsa nʼcholinga choti ukhalebe wodzipereka kwa Mulungu.

  • 2 Timoteyo 4:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chifukwa idzafika nthawi imene anthu sadzafunanso kuphunzitsidwa zolondola,+ koma mogwirizana ndi zimene amalakalaka, adzapeza aphunzitsi oti aziwauza zowakomera mʼkhutu.+ 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi nʼkumamvetsera nkhani zonama.

  • Tito 1:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Umboni umenewu ndi woona. Chifukwa cha zimenezi, pitiriza kuwadzudzula mwamphamvu kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba. 14 Asamamvetsere nthano zachiyuda ndiponso kutsatira malamulo a anthu amene asiya choonadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena