Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+

  • 1 Petulo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu+ zomwe zili mʼmanja mwanu. Monga oyangʼanira, muzigwira ntchito yanu, osati mokakamizika koma mofunitsitsa monga atumiki a Mulungu.+ Muziigwira ndi mtima wonse, osati chifukwa chofuna kupindulapo kenakake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena