Agalatiya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ngati munthu ali wogwirizana ndi Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa kumakhala kopanda ntchito.+ Koma chofunika kwambiri nʼkukhala ndi chikhulupiriro chimene chimaonekera posonyeza chikondi.
6 Chifukwa ngati munthu ali wogwirizana ndi Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa kumakhala kopanda ntchito.+ Koma chofunika kwambiri nʼkukhala ndi chikhulupiriro chimene chimaonekera posonyeza chikondi.