Aroma 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu.
3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu.