2 Timoteyo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho usachite manyazi ndi ntchito yolalikira za Ambuye wathu,+ kapena kuchita manyazi ndi ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye. Koma khala wokonzeka kuvutika+ chifukwa cha uthenga wabwino ndipo uzidalira mphamvu ya Mulungu.+
8 Choncho usachite manyazi ndi ntchito yolalikira za Ambuye wathu,+ kapena kuchita manyazi ndi ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye. Koma khala wokonzeka kuvutika+ chifukwa cha uthenga wabwino ndipo uzidalira mphamvu ya Mulungu.+