Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo.

  • Aefeso 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho ndikukupemphani kuti musafooke poona mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, popeza mavuto amene ndikukumana nawowa achititsa kuti mulandire ulemerero.+

  • Akolose 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena