Yohane 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yudasi atalandira mkatewo, Satana analowa mwa iye.+ Choncho Yesu anamuuza kuti: “Zimene wakonza kuti uchite, zichite mwamsanga.” Machitidwe 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Petulo anati: “Hananiya, nʼchifukwa chiyani Satana wakulimbitsa mtima kuti unamize+ mzimu woyera+ nʼkubisa ndalama zina za mundawo? 1 Timoteyo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ena mwa anthuwa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda, ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa, aphunzirepo kanthu nʼkusiya kunyoza Mulungu.
27 Yudasi atalandira mkatewo, Satana analowa mwa iye.+ Choncho Yesu anamuuza kuti: “Zimene wakonza kuti uchite, zichite mwamsanga.”
3 Koma Petulo anati: “Hananiya, nʼchifukwa chiyani Satana wakulimbitsa mtima kuti unamize+ mzimu woyera+ nʼkubisa ndalama zina za mundawo?
20 Ena mwa anthuwa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda, ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa, aphunzirepo kanthu nʼkusiya kunyoza Mulungu.