Yohane 5:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+ Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+