Yohane 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atate saweruza munthu aliyense, koma wapereka udindo wonse woweruza kwa Mwana,+