Salimo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipulumutseni mʼkamwa mwa mkango+ komanso kunyanga za ngʼombe zamphongo zamʼtchire.Mundiyankhe ndi kundipulumutsa.
21 Ndipulumutseni mʼkamwa mwa mkango+ komanso kunyanga za ngʼombe zamphongo zamʼtchire.Mundiyankhe ndi kundipulumutsa.