Aroma 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mundiperekere moni kwa Purisika ndi Akula,+ antchito anzanga potumikira Khristu Yesu.