-
Yakobo 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ngati alipo asonyeze zimenezi pochita zinthu zabwino pa moyo wake. Azichita zinthu zonse mofatsa, lomwe ndi khalidwe limene limabwera chifukwa cha nzeru.
-