Yohane 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Yesu anayankha kuti: “Ngati ndikudzilemekeza ndekha, ndiye kuti ulemerero wanga ndi wopanda pake. Atate wanga ndi amene amandilemekeza,+ amene inu mukunena kuti ndi Mulungu wanu.
54 Yesu anayankha kuti: “Ngati ndikudzilemekeza ndekha, ndiye kuti ulemerero wanga ndi wopanda pake. Atate wanga ndi amene amandilemekeza,+ amene inu mukunena kuti ndi Mulungu wanu.