Aefeso 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho tisakhalenso ana. Tisamatengeketengeke ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde ndiponso tisamatengeke kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya zinthu zachinyengo zimene anthu amaphunzitsa+ popeka mabodza mochenjera.
14 Choncho tisakhalenso ana. Tisamatengeketengeke ngati kuti tikukankhidwa ndi mafunde ndiponso tisamatengeke kupita uku ndi uku ndi mphepo iliyonse ya zinthu zachinyengo zimene anthu amaphunzitsa+ popeka mabodza mochenjera.