Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa adzalamula angelo ake+ zokhudza iwe,Kuti akuteteze mʼnjira zako zonse.+ Luka 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atatero mngelo wochokera kumwamba anaonekera kwa iye nʼkumulimbikitsa.+