Mateyu 27:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka ndipo matanthwe anangʼambika.
51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka ndipo matanthwe anangʼambika.