Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+

  • Akolose 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma mukuyenera kupitiriza kukhala mogwirizana ndi chikhulupiriro chanu,+ muli okhazikika pamaziko,+ muli olimba+ komanso muli osasunthika pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva, umenenso unalalikidwa padziko lonse.*+ Ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wa uthenga wabwino umenewu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena