Genesis 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, kenako anayamba kuseka nʼkunena mumtima mwake kuti:+ “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+ Genesis 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Sara anakhala woyembekezera+ ndipo anaberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika ndendende pa nthawi imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+
17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, kenako anayamba kuseka nʼkunena mumtima mwake kuti:+ “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+
2 Choncho Sara anakhala woyembekezera+ ndipo anaberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika ndendende pa nthawi imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+