Ekisodo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mkaziyo anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ataona kuti mwanayo ndi wokongola, anamubisa kwa miyezi itatu.+
2 Mkaziyo anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ataona kuti mwanayo ndi wokongola, anamubisa kwa miyezi itatu.+