Ekisodo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+
10 Mwana uja atakula, anapita naye kwa mwana wa Farao, ndipo anakhala mwana wake.+ Zitatero anamʼpatsa dzina lakuti Mose* nʼkunena kuti: “Chifukwa chakuti ndinamuvuula mʼmadzi.”+