Oweruza 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi anali msilikali wamphamvu. Mayi ake anali hule, ndipo bambo ake anali Giliyadi.
11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi anali msilikali wamphamvu. Mayi ake anali hule, ndipo bambo ake anali Giliyadi.