Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zedekiya mwana wa Kenaana anapita pomwe panali Mikaya nʼkumumenya mbama ndipo ananena kuti: “Zingatheke bwanji kuti mzimu wa Yehova undidutse nʼkukalankhula ndi iwe?”+

  • Yeremiya 38:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho iwo anagwira Yeremiya nʼkumuponya mʼchitsime cha Malikiya mwana wa mfumu, chimene chinali mʼBwalo la Alonda.+ Iwo analowetsa Yeremiya mʼchitsimemo pogwiritsa ntchito zingwe. Mʼchitsimemo munalibe madzi koma munali matope ndipo Yeremiya anayamba kumira mʼmatopemo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena