Akolose 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndi chifaniziro cha Mulungu wosaonekayo,+ woyamba kubadwa wa chilengedwe chonse.+