Yeremiya 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma inu Yehova, mukundidziwa bwino+ ndipo mumandiona.Mwafufuza mtima wanga ndipo mwapeza kuti ndine wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,Ndipo muwaike padera poyembekezera tsiku limene adzaphedwe.
3 Koma inu Yehova, mukundidziwa bwino+ ndipo mumandiona.Mwafufuza mtima wanga ndipo mwapeza kuti ndine wokhulupirika kwa inu.+ Apatuleni ngati nkhosa zimene zikukaphedwa,Ndipo muwaike padera poyembekezera tsiku limene adzaphedwe.