Deuteronomo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndidzakupatsaninso mvula pa nthawi yake mʼdziko lanu, mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ndipo mudzakolola mbewu zanu nʼkukhala ndi vinyo watsopano komanso mafuta.+ Yeremiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mumtima mwawo sanena kuti: “Tiyeni tsopano tiope Yehova Mulungu wathu,Amene amatigwetsera mvula mʼnyengo yake,Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira,Amene amaonetsetsa kuti tikukolola pa nthawi yake.”*+
14 ndidzakupatsaninso mvula pa nthawi yake mʼdziko lanu, mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ndipo mudzakolola mbewu zanu nʼkukhala ndi vinyo watsopano komanso mafuta.+
24 Mumtima mwawo sanena kuti: “Tiyeni tsopano tiope Yehova Mulungu wathu,Amene amatigwetsera mvula mʼnyengo yake,Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira,Amene amaonetsetsa kuti tikukolola pa nthawi yake.”*+