Yakobo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso, chilungamo ndi chipatso chimene anthu obweretsa mtendere+ amafesa mumtendere.+