1 Akorinto 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale, musakhale ana aangʼono pa nkhani yomvetsa zinthu.+ Koma khalani ana pa zoipa,+ ndipo pa nkhani yomvetsa zinthu khalani anthu akuluakulu.+ Aefeso 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mpaka tonse tidzakhale ogwirizana pa zimene timakhulupirira komanso podziwa molondola Mwana wa Mulungu. Zikadzatero, tidzakhala anthu achikulire, amene afika pa msinkhu wa munthu wamkulu+ ngati mmene Khristu analili.
20 Abale, musakhale ana aangʼono pa nkhani yomvetsa zinthu.+ Koma khalani ana pa zoipa,+ ndipo pa nkhani yomvetsa zinthu khalani anthu akuluakulu.+
13 mpaka tonse tidzakhale ogwirizana pa zimene timakhulupirira komanso podziwa molondola Mwana wa Mulungu. Zikadzatero, tidzakhala anthu achikulire, amene afika pa msinkhu wa munthu wamkulu+ ngati mmene Khristu analili.