1 Akorinto 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera, yomvetsa zinsinsi zonse zopatulika komanso yodziwa zinthu zonse,+ ndipo ndili ndi chikhulupiriro cholimba moti ndingathe kusuntha mapiri, koma ndilibe chikondi, zomwe ndimachita zilibe ntchito.+
2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera, yomvetsa zinsinsi zonse zopatulika komanso yodziwa zinthu zonse,+ ndipo ndili ndi chikhulupiriro cholimba moti ndingathe kusuntha mapiri, koma ndilibe chikondi, zomwe ndimachita zilibe ntchito.+