Genesis 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe nʼkuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo nʼkumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+ Genesis 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mngeloyo anati: “Usamuvulaze mwanayo ndipo usamuchite chilichonse. Tsopano ndadziwa kuti umaopa Mulungu, chifukwa sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+
9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe nʼkuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo nʼkumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+
12 Ndiyeno mngeloyo anati: “Usamuvulaze mwanayo ndipo usamuchite chilichonse. Tsopano ndadziwa kuti umaopa Mulungu, chifukwa sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+