2 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu wathu, kodi si paja munathamangitsa anthu amene ankakhala mʼdzikoli pamaso pa anthu anu Aisiraeli nʼkulipereka kwa mbadwa* za Abulahamu, bwenzi lanu, kuti likhale lawo mpaka kalekale?+ Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+Iwe Yakobo, amene ndakusankha,+Mbadwa* ya mnzanga Abulahamu.+
7 Inu Mulungu wathu, kodi si paja munathamangitsa anthu amene ankakhala mʼdzikoli pamaso pa anthu anu Aisiraeli nʼkulipereka kwa mbadwa* za Abulahamu, bwenzi lanu, kuti likhale lawo mpaka kalekale?+
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+Iwe Yakobo, amene ndakusankha,+Mbadwa* ya mnzanga Abulahamu.+