1 Mafumu 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anthu anu akakuchimwirani (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu nʼkuwakwiyira kwambiri ndiponso kuwapereka kwa adani, adani awowo nʼkuwatenga kupita nawo kudziko lakutali kapena lapafupi,+ Miyambo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndi ndani anganene kuti: “Ndayeretsa mtima wanga.+Ndine woyera ku tchimo langa”?+ 1 Yohane 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikamanena kuti, “Tilibe uchimo,” ndiye kuti tikudzinamiza+ ndipo mumtima mwathu mulibe choonadi.
46 Anthu anu akakuchimwirani (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu nʼkuwakwiyira kwambiri ndiponso kuwapereka kwa adani, adani awowo nʼkuwatenga kupita nawo kudziko lakutali kapena lapafupi,+