Mateyu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pitirizani kupempha ndipo adzakupatsani.+ Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+
7 Pitirizani kupempha ndipo adzakupatsani.+ Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+