1 Atesalonika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+ Yakobo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma nzeru yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+
13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+
17 Koma nzeru yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+