2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+ Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,*+ chifukwa pochita zimenezi, ena anachereza angelo mosadziwa.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+