2 Timoteyo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nʼchifukwa chake ndikuvutika chonchi,+ koma sindikuchita manyazi.+ Ndikudziwa amene ndikumukhulupirira, ndipo sindikukayikira kuti adzateteza zonse zimene ndamupatsa mpaka tsiku lachiweruzo.+
12 Nʼchifukwa chake ndikuvutika chonchi,+ koma sindikuchita manyazi.+ Ndikudziwa amene ndikumukhulupirira, ndipo sindikukayikira kuti adzateteza zonse zimene ndamupatsa mpaka tsiku lachiweruzo.+