Afilipi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.
17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.