-
2 Atesalonika 2:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Komanso Ambuye wathu Yesu Khristu ndiponso Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo salephera kutilimbikitsa komanso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ kudzera mwa kukoma mtima kwakukulu, 17 alimbikitse mitima yanu ndi kukulimbikitsani kuti nthawi zonse muzichita komanso kulankhula zinthu zabwino.
-