Deuteronomo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakupangani kukhala anthu ake oyera,+ mogwirizana ndi zimene analumbira kwa inu,+ chifukwa mukupitiriza kusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu ndipo mukuyenda mʼnjira zake. Aroma 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho abale, ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe yamoyo, yoyera+ ndiponso yovomerezeka kwa Mulungu, yomwe ndi utumiki wopatulika pogwiritsa ntchito luso la kuganiza.+ Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.
9 Yehova adzakupangani kukhala anthu ake oyera,+ mogwirizana ndi zimene analumbira kwa inu,+ chifukwa mukupitiriza kusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu ndipo mukuyenda mʼnjira zake.
12 Choncho abale, ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe yamoyo, yoyera+ ndiponso yovomerezeka kwa Mulungu, yomwe ndi utumiki wopatulika pogwiritsa ntchito luso la kuganiza.+
14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.