Yohane 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+ Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anatisankha kuti tikakhale ogwirizana ndi Khristu dziko lisanakhazikitsidwe nʼcholinga choti tizisonyeza chikondi komanso kuti tikhale oyera ndiponso opanda chilema+ pamaso pa Mulungu.
5 Ndiye tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+
4 Iye anatisankha kuti tikakhale ogwirizana ndi Khristu dziko lisanakhazikitsidwe nʼcholinga choti tizisonyeza chikondi komanso kuti tikhale oyera ndiponso opanda chilema+ pamaso pa Mulungu.