Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,* Aheberi 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+
22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*
24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+