Agalatiya 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa zimene thupi limalakalaka zimalimbana ndi mzimu ndipo mzimu nawonso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana kuti musachite zinthu zimene mumafuna kuchita.+ Yakobo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi nkhondo ndi ndewu zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Kodi sizikuchokera mʼzilakolako za thupi lanu zimene zikulimbana kuti zizilamulira matupi anu?*+
17 Chifukwa zimene thupi limalakalaka zimalimbana ndi mzimu ndipo mzimu nawonso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana kuti musachite zinthu zimene mumafuna kuchita.+
4 Kodi nkhondo ndi ndewu zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Kodi sizikuchokera mʼzilakolako za thupi lanu zimene zikulimbana kuti zizilamulira matupi anu?*+