Aroma 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense azimvera olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali mʼmaudindo awo osiyanasiyana mololedwa ndi Mulungu.+ Aefeso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza kuchokera pansi pa mtima, ngati mmene mumachitira ndi Khristu. Tito 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino.
13 Munthu aliyense azimvera olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali mʼmaudindo awo osiyanasiyana mololedwa ndi Mulungu.+
5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza kuchokera pansi pa mtima, ngati mmene mumachitira ndi Khristu.
3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino.